Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku
Baibulo labwino zedi, lokhala ndi zithunzi zoonetsa zimene zikuchitika, tsopano latanthauzidwa m’chinenero chanu:

Nsembe. Nkhondo. Mayesero. Chiwembu. Chiyembekezo. Chipulumutso.

Mulungu anasankha kudzivumbulutsa yekha kwa anthu, osati kudzera mu mfundo zokhazikika chabe, kapena m’nzeru chabe, kapenanso m’ziphunzitso chabe, koma makamaka kudzera m’nkhani za uneneri, nkhondo, chifundo, chiweruzo, zozizwitsa, imfa, moyo, ndi chikhululukiro.
Nkhani ya mmene Mulungu anakonzera kupulumutsa anthu yafotokozedwa mwatsatanetsatane kuchokera m’buku la Genesis mpaka Chivumbulutso. Iwo amene adaonapo mmene buku la Marvel Comic lidalembedwera, akukondwera kwambiri ndi ntchito yopatsa chidwi imene ili m’buku la Zabwino ndi Zoipa. Zithunzi zake ndi zapamwamba kwambiri komanso zopatsa chidwi.
Inde, Baibulo lotchuka zedi, lokhala ndi zithunzi, lotchedwa Zabwino ndi Zoipa, latanthauzidwa tsopano m’chinenero chanu! Buku limeneli limakuthandizani kudziwa mwatsatenetsatane nkhani yonse ya m’Baibulo mosavuta. Limaonetsa nkhani zikukuzikulu m’njira yosavuta kutsatira yonga ngati sewero. Pansi pa tsamba lililonse pali kalozera wa m’Buku Lopatulika kuti inu owerenga muthe kuwerenga nkhani yonsewo m’Baibulo. Bulu lapamwambali, lolembedwa ngati sewero, lili ndi masamba 320 okhala ndi nkhani za m’Baibulo.
Good and Evil Comic Book. Chichewa comic book. Christian comic book in Chichewa language.

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 1

CHIYAMBI

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 2

ABRAHAMU NDI ISAKI

http://cdn.goodandevilbook.com/chichewa/Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 3

MOSE

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 4

EKSODO

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 5

ANENERI

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 6

UNENERI WOKHUDZA KHRISTU

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 7

CHIPANGANO CHATSOPANO, KUBADWA KWA KHRISTU, NDI MAYESERO AKE

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 8

UTUMIKI WOYAMBIRIRA

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 9

ZOZIZWITSA NDI MAFANIZO

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 10

PASKHA NDI MASAUTSO KHRISTU

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 11

KUUKA KWA AKUFA NDI MPINGO WOYAMBIRIRA

Zabwino ndi Zoipa Chosseketsa Buku Mutu chithunzi

MUTU 12

KU DZIKO LONSE LAPANSI

This site accelerated by the cdn77 network.